Genesis 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Onsewa anagwirizana+ ndi kutsetserekera limodzi kuchigwa cha Sidimu,+ ku Nyanja Yamchere.+