Salimo 83:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kuti anthu adziwe+ kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+Inu nokha ndinu Wam’mwambamwamba,+ wolamulira dziko lonse lapansi.+ Aheberi 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 chifukwa watchulidwa mwachindunji ndi Mulungu kuti ndi mkulu wa ansembe monga mwa unsembe wa Melekizedeki.+
18 Kuti anthu adziwe+ kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+Inu nokha ndinu Wam’mwambamwamba,+ wolamulira dziko lonse lapansi.+
10 chifukwa watchulidwa mwachindunji ndi Mulungu kuti ndi mkulu wa ansembe monga mwa unsembe wa Melekizedeki.+