Genesis 28:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mwala wachikumbutso umene ndauimika panowu, udzakhala nyumba ya Mulungu.+ Pa chilichonse chimene mudzandipatsa, sindidzalephera kukubwezerani chakhumi chake.”+ Aheberi 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho mungaone kuti munthuyu anali wofunika kwambiri. Moti ngakhale kholo lathu Abulahamu, linapereka kwa iye chakhumi pa zinthu zabwino kwambiri zimene anafunkha.+
22 Mwala wachikumbutso umene ndauimika panowu, udzakhala nyumba ya Mulungu.+ Pa chilichonse chimene mudzandipatsa, sindidzalephera kukubwezerani chakhumi chake.”+
4 Choncho mungaone kuti munthuyu anali wofunika kwambiri. Moti ngakhale kholo lathu Abulahamu, linapereka kwa iye chakhumi pa zinthu zabwino kwambiri zimene anafunkha.+