Esitere 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Ayuda amene anali ku Susani anasonkhananso pamodzi pa tsiku la 14+ la mwezi wa Adara, ndipo anapha amuna 300 ku Susani, koma sanafunkhe zinthu zawo.+
15 Ndiyeno Ayuda amene anali ku Susani anasonkhananso pamodzi pa tsiku la 14+ la mwezi wa Adara, ndipo anapha amuna 300 ku Susani, koma sanafunkhe zinthu zawo.+