Ekisodo 31:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chimenechi n’chizindikiro pakati pa ine ndi ana a Isiraeli mpaka kalekale,+ chifukwa m’masiku 6, Yehova anapanga kumwamba ndi dziko lapansi, ndipo pa tsiku la 7 anapuma pa ntchito yake.’”+ Aheberi 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti penapake, ponena za tsiku la 7, anati: “Ndipo Mulungu anapuma pa ntchito zake zonse pa tsiku la 7.”+
17 Chimenechi n’chizindikiro pakati pa ine ndi ana a Isiraeli mpaka kalekale,+ chifukwa m’masiku 6, Yehova anapanga kumwamba ndi dziko lapansi, ndipo pa tsiku la 7 anapuma pa ntchito yake.’”+
4 Pakuti penapake, ponena za tsiku la 7, anati: “Ndipo Mulungu anapuma pa ntchito zake zonse pa tsiku la 7.”+