1 Samueli 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mkazi mnzake wa Hana anali kum’sautsa+ kwambiri n’cholinga choti amukhumudwitse, chifukwa chakuti Yehova anali atatseka mimba yake.
6 Mkazi mnzake wa Hana anali kum’sautsa+ kwambiri n’cholinga choti amukhumudwitse, chifukwa chakuti Yehova anali atatseka mimba yake.