Genesis 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Isaki atakwanitsa masiku 8, Abulahamu anamudula mwana wakeyo, monga mmene Mulungu anamulamulira.+ Luka 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano masiku 8+ atakwanira kuti achite mdulidwe+ wa mwanayo, anamupatsanso dzina lakuti Yesu.+ Dzina limeneli ndi limene mngelo uja anatchula m’mbuyomo, Mariya asanakhale ndi pakati.+ Afilipi 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ineyo ndinadulidwa pa tsiku la 8,+ ndine wa mtundu wa Isiraeli, wa fuko la Benjamini,+ Mheberi wobadwa kwa Aheberi.+ Kunena za chilamulo, ndine Mfarisi.+
21 Tsopano masiku 8+ atakwanira kuti achite mdulidwe+ wa mwanayo, anamupatsanso dzina lakuti Yesu.+ Dzina limeneli ndi limene mngelo uja anatchula m’mbuyomo, Mariya asanakhale ndi pakati.+
5 Ineyo ndinadulidwa pa tsiku la 8,+ ndine wa mtundu wa Isiraeli, wa fuko la Benjamini,+ Mheberi wobadwa kwa Aheberi.+ Kunena za chilamulo, ndine Mfarisi.+