Mateyu 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yesu anawayang’anitsitsa n’kunena kuti: “Kwa anthu zimenezi n’zosathekadi, koma zinthu zonse n’zotheka kwa Mulungu.”+ Luka 1:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Izi zachitika chifukwa zimene Mulungu wanena, sizilephereka.”+
26 Yesu anawayang’anitsitsa n’kunena kuti: “Kwa anthu zimenezi n’zosathekadi, koma zinthu zonse n’zotheka kwa Mulungu.”+