1 Atesalonika 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti ogona+ amagona usiku,+ ndipo amene amaledzera amakonda kuledzera usiku.