Levitiko 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Usavule bambo ako+ ndi mayi ako. Amenewo ndi mayi ako. Usawavule. Ezekieli 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu avula bambo awo.+ Iwo agona ndi mkazi wodetsedwa amene akusamba.+