Genesis 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako Abulahamu anabwerera kwa anyamata ake aja, n’kunyamukira nawo limodzi kubwerera ku Beere-seba.+ Abulahamu anapitirizabe kukhala ku Beere-seba.
19 Kenako Abulahamu anabwerera kwa anyamata ake aja, n’kunyamukira nawo limodzi kubwerera ku Beere-seba.+ Abulahamu anapitirizabe kukhala ku Beere-seba.