-
Genesis 16:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Pamene Hagara anaberekera Abulamu Isimaeli, Abulamuyo n’kuti ali ndi zaka 86.
-
-
Genesis 21:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Abulahamu anali ndi zaka 100 pamene mwana wake Isaki anabadwa.
-