Genesis 26:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma iwo anayankha kuti: “Ife taona kuti ndithu Yehova ali nawe.+ Choncho tinaganiza zokupempha kuti, ‘Chonde, tiye tilumbirirane,+ iwe ndi ife, ndipo tichite nawe pangano.+
28 Koma iwo anayankha kuti: “Ife taona kuti ndithu Yehova ali nawe.+ Choncho tinaganiza zokupempha kuti, ‘Chonde, tiye tilumbirirane,+ iwe ndi ife, ndipo tichite nawe pangano.+