Genesis 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anatenga mkazi wake Sarai,+ Loti mwana wa m’bale wake,+ ndi chuma chawo chonse,+ komanso akapolo awo onse amene anapeza kudziko la Harana. Iwo ananyamuka ulendo wopita kudziko la Kanani.+ Potsirizira pake anafika ku Kanani. Machitidwe 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo anasamuka m’dziko la Akasidi ndi kukakhala ku Harana. Kumeneko, pambuyo pa imfa ya bambo ake,+ Mulungu anamuuza kuti asamukire m’dziko lino limene inu mukukhala tsopano.+
5 Iye anatenga mkazi wake Sarai,+ Loti mwana wa m’bale wake,+ ndi chuma chawo chonse,+ komanso akapolo awo onse amene anapeza kudziko la Harana. Iwo ananyamuka ulendo wopita kudziko la Kanani.+ Potsirizira pake anafika ku Kanani.
4 Pamenepo anasamuka m’dziko la Akasidi ndi kukakhala ku Harana. Kumeneko, pambuyo pa imfa ya bambo ake,+ Mulungu anamuuza kuti asamukire m’dziko lino limene inu mukukhala tsopano.+