Salimo 118:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Umenewu wachokera kwa Yehova,+Ndipo ndi wodabwitsa m’maso mwathu.+ Maliko 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi simunawerenge kuti ‘Umenewu wachokera kwa Yehova, ndipo ndi wodabwitsa m’maso mwathu’?”+