Ekisodo 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Ndipo izi ndizo zigamulo zoti uwaikire:+ Deuteronomo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Tsopano inu Aisiraeli, mverani malangizo ndi zigamulo zimene ndikukuphunzitsani kuti muzitsatira. Mukatero mudzakhala ndi moyo+ n’kukalowa m’dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu akukupatsani, ndi kukalitenga kukhala lanu. Aheberi 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma tsopano Yesu walandira ntchito yapamwamba kwambiri yotumikira ena, moti wakhalanso mkhalapakati+ wa pangano labwino kwambiri,+ limene lakhazikitsidwa mwalamulo pa malonjezo abwinonso.+
4 “Tsopano inu Aisiraeli, mverani malangizo ndi zigamulo zimene ndikukuphunzitsani kuti muzitsatira. Mukatero mudzakhala ndi moyo+ n’kukalowa m’dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu akukupatsani, ndi kukalitenga kukhala lanu.
6 Koma tsopano Yesu walandira ntchito yapamwamba kwambiri yotumikira ena, moti wakhalanso mkhalapakati+ wa pangano labwino kwambiri,+ limene lakhazikitsidwa mwalamulo pa malonjezo abwinonso.+