Ekisodo 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yoswa anachitadi zimene Mose anamuuza,+ kuti amenyane ndi Aamaleki. Mose, Aroni ndi Hura+ anapita pamwamba pa phiri.
10 Yoswa anachitadi zimene Mose anamuuza,+ kuti amenyane ndi Aamaleki. Mose, Aroni ndi Hura+ anapita pamwamba pa phiri.