Ekisodo 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Koma iwe, ulamule ana a Isiraeli kuti akupezere mafuta ounikira oyenga bwino kwambiri a maolivi, kuti nyale ziziyaka nthawi zonse.+
20 “Koma iwe, ulamule ana a Isiraeli kuti akupezere mafuta ounikira oyenga bwino kwambiri a maolivi, kuti nyale ziziyaka nthawi zonse.+