Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 29:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Choncho ndidzakhala pakati pa ana a Isiraeli, ndipo ndidzakhala Mulungu wawo.+

  • 1 Mafumu 6:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndidzakhaladi pakati pa ana a Isiraeli,+ ndipo sindidzasiya anthu anga, Aisiraeli.”+

  • Aheberi 9:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Komabe, pamene Khristu anabwera monga mkulu wa ansembe,+ wa zinthu zabwino zimene zakwaniritsidwa, anatero kudzera m’chihema chachikulu ndi changwiro kwambiri chimene sichinapangidwe ndi manja a anthu, kutanthauza kuti, sichili mbali ya chilengedwe chapansi pano.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena