Ekisodo 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno ulikute ndi golide woyenga bwino pamwamba pake, ndi m’mbali mwake kuzungulira guwalo, komanso nyanga zake. Upange mkombero wagolide kuzungulira guwa lonselo.+
3 Ndiyeno ulikute ndi golide woyenga bwino pamwamba pake, ndi m’mbali mwake kuzungulira guwalo, komanso nyanga zake. Upange mkombero wagolide kuzungulira guwa lonselo.+