1 Samueli 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Motero anthuwo anatumiza anthu ku Silo kukatenga likasa la pangano la Yehova wa makamu, amene akukhala pa akerubi.+ Ndipo Hofeni ndi Pinihasi, ana awiri a Eli, anali pamenepo ndi likasa la pangano la Mulungu woona.+ Aheberi 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma pamwamba pa likasalo panali akerubi aulemerero+ amene zithunzithunzi zawo zinali kugwera pachivundikiro chophimba machimo.+ Koma ino si nthawi yofotokoza zinthu zimenezi mwatsatanetsatane.
4 Motero anthuwo anatumiza anthu ku Silo kukatenga likasa la pangano la Yehova wa makamu, amene akukhala pa akerubi.+ Ndipo Hofeni ndi Pinihasi, ana awiri a Eli, anali pamenepo ndi likasa la pangano la Mulungu woona.+
5 Koma pamwamba pa likasalo panali akerubi aulemerero+ amene zithunzithunzi zawo zinali kugwera pachivundikiro chophimba machimo.+ Koma ino si nthawi yofotokoza zinthu zimenezi mwatsatanetsatane.