Ekisodo 39:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako anapanga efodi*+ wagolide, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri.
2 Kenako anapanga efodi*+ wagolide, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri.