Ekisodo 39:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anapanga chovala pachifuwa+ ndipo anachipanga mwaluso mofanana ndi efodi. Chinali chagolide, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri.+
8 Kenako anapanga chovala pachifuwa+ ndipo anachipanga mwaluso mofanana ndi efodi. Chinali chagolide, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri.+