1 Mafumu 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Choncho Eliya anatenga miyala 12 mogwirizana ndi chiwerengero cha mafuko a ana a Yakobo, yemwe mawu a Yehova anam’fikira,+ akuti: “Dzina lako lidzakhala Isiraeli.”+
31 Choncho Eliya anatenga miyala 12 mogwirizana ndi chiwerengero cha mafuko a ana a Yakobo, yemwe mawu a Yehova anam’fikira,+ akuti: “Dzina lako lidzakhala Isiraeli.”+