Ekisodo 39:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Anawombanso lamba wa pamimba+ ndi ulusi wopota wabwino kwambiri, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira ndi ulusi wofiira kwambiri, monga mmene Yehova analamulira Mose.
29 Anawombanso lamba wa pamimba+ ndi ulusi wopota wabwino kwambiri, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira ndi ulusi wofiira kwambiri, monga mmene Yehova analamulira Mose.