Levitiko 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Musamadye mafuta kapena magazi+ alionse. Limeneli ndi lamulo ku mibadwo yanu yonse mpaka kalekale,* kulikonse kumene mungakhale.’” Levitiko 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Koma mafuta onse a ng’ombe ya nsembe yamachimo, aziwachotsa. Azichotsa mafuta okuta matumbo, mafuta onse okuta matumbo.+ Salimo 69:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti kudzipereka kwambiri panyumba yanu kwandidya,+Ndipo mnyozo wa anthu amene akukutonzani wagwa pa ine.+
17 “‘Musamadye mafuta kapena magazi+ alionse. Limeneli ndi lamulo ku mibadwo yanu yonse mpaka kalekale,* kulikonse kumene mungakhale.’”
8 “‘Koma mafuta onse a ng’ombe ya nsembe yamachimo, aziwachotsa. Azichotsa mafuta okuta matumbo, mafuta onse okuta matumbo.+
9 Pakuti kudzipereka kwambiri panyumba yanu kwandidya,+Ndipo mnyozo wa anthu amene akukutonzani wagwa pa ine.+