Levitiko 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Matumbo+ ake ndi ziboda zake azizitsuka ndi madzi. Akatero ansembe azitentha* nyama yonse paguwa lansembe kuti ikhale nsembe yopsereza. Imeneyi ndi nsembe yotentha ndi moto, yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.+ Levitiko 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atatero, anatsuka matumbo ndi ziboda, n’kuzitentha paguwa lansembe+ pamwamba pa nsembe yopsereza.
9 Matumbo+ ake ndi ziboda zake azizitsuka ndi madzi. Akatero ansembe azitentha* nyama yonse paguwa lansembe kuti ikhale nsembe yopsereza. Imeneyi ndi nsembe yotentha ndi moto, yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.+