Levitiko 16:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Koma ng’ombe yamphongo ya nsembe yamachimo ndi mbuzi ya nsembe yamachimo zimene magazi ake analowa nawo m’malo oyera pokaphimba machimo, azizitulutsira kunja kwa msasa ndipo azitentha pamoto zikopa zake, nyama ndi ndowe zake.+
27 “Koma ng’ombe yamphongo ya nsembe yamachimo ndi mbuzi ya nsembe yamachimo zimene magazi ake analowa nawo m’malo oyera pokaphimba machimo, azizitulutsira kunja kwa msasa ndipo azitentha pamoto zikopa zake, nyama ndi ndowe zake.+