Levitiko 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Atatero anabweretsa nkhosa yamphongo yachiwiri, nkhosa yolongera unsembe,+ ndipo Aroni ndi ana ake anaika manja awo pamutu pa nkhosayo.
22 Atatero anabweretsa nkhosa yamphongo yachiwiri, nkhosa yolongera unsembe,+ ndipo Aroni ndi ana ake anaika manja awo pamutu pa nkhosayo.