Ekisodo 37:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kumbali ziwiri za guwalo anapangako mphete zagolide, ziwiri kumbali iyi ndi zinanso ziwiri kumbali inayo. Anazipanga m’munsi mwa mkombero kuti muzilowa mitengo yonyamulira guwalo.+
27 Kumbali ziwiri za guwalo anapangako mphete zagolide, ziwiri kumbali iyi ndi zinanso ziwiri kumbali inayo. Anazipanga m’munsi mwa mkombero kuti muzilowa mitengo yonyamulira guwalo.+