Yesaya 54:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana ako onse+ adzakhala anthu ophunzitsidwa ndi Yehova,+ ndipo mtendere wa ana ako udzakhala wochuluka.+ 1 Akorinto 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 kuti mwa iye mwakhala olemera+ m’zinthu zonse, pokhala ndi mphamvu zonse za kulankhula ndi kudziwa zinthu zonse,+ 2 Akorinto 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Sitinganene kuti ndife oyenera kugwira ntchito imeneyi chifukwa cha mphamvu zathu,+ koma ndife oyenera kugwira ntchito imeneyi chifukwa cha Mulungu,+
13 Ana ako onse+ adzakhala anthu ophunzitsidwa ndi Yehova,+ ndipo mtendere wa ana ako udzakhala wochuluka.+
5 kuti mwa iye mwakhala olemera+ m’zinthu zonse, pokhala ndi mphamvu zonse za kulankhula ndi kudziwa zinthu zonse,+
5 Sitinganene kuti ndife oyenera kugwira ntchito imeneyi chifukwa cha mphamvu zathu,+ koma ndife oyenera kugwira ntchito imeneyi chifukwa cha Mulungu,+