Levitiko 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pomalizira, Mose anathira ena mwa mafuta odzozera pamutu pa Aroni ndi kum’dzoza kuti akhale wopatulika.+ Machitidwe 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Nkhani yake inali yonena za Yesu wa ku Nazareti, kuti Mulungu anamudzoza ndi mzimu woyera+ ndi mphamvu. Ndiponso kuti popeza Mulungu anali naye,+ anayendayenda m’dziko, n’kumachita zabwino ndi kuchiritsa onse osautsidwa ndi Mdyerekezi.+
12 Pomalizira, Mose anathira ena mwa mafuta odzozera pamutu pa Aroni ndi kum’dzoza kuti akhale wopatulika.+
38 Nkhani yake inali yonena za Yesu wa ku Nazareti, kuti Mulungu anamudzoza ndi mzimu woyera+ ndi mphamvu. Ndiponso kuti popeza Mulungu anali naye,+ anayendayenda m’dziko, n’kumachita zabwino ndi kuchiritsa onse osautsidwa ndi Mdyerekezi.+