Levitiko 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Wonyoza dzina la Yehova aziphedwa ndithu.+ Khamu lonse lizim’ponya miyala. Kaya ndi mlendo wokhala pakati panu kapena nzika, aziphedwa chifukwa chonyoza Dzinalo.+ Numeri 15:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pambuyo pake Yehova anauza Mose kuti: “Munthuyo aphedwe basi!+ Khamu lonselo likam’ponye miyala kunja kwa msasa.”+
16 Wonyoza dzina la Yehova aziphedwa ndithu.+ Khamu lonse lizim’ponya miyala. Kaya ndi mlendo wokhala pakati panu kapena nzika, aziphedwa chifukwa chonyoza Dzinalo.+
35 Pambuyo pake Yehova anauza Mose kuti: “Munthuyo aphedwe basi!+ Khamu lonselo likam’ponye miyala kunja kwa msasa.”+