Genesis 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 n’kumuuza kuti: “Yehova wati, ‘Ndikulumbira+ pali dzina langa, kuti chifukwa cha zimene wachitazi, posakana kupereka mwana wako yekhayo,+ Aheberi 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamene Mulungu analonjeza Abulahamu,+ analumbira pa dzina lake+ chifukwa panalibe wina wamkulu kwa iye amene akanamulumbirira.
16 n’kumuuza kuti: “Yehova wati, ‘Ndikulumbira+ pali dzina langa, kuti chifukwa cha zimene wachitazi, posakana kupereka mwana wako yekhayo,+
13 Pamene Mulungu analonjeza Abulahamu,+ analumbira pa dzina lake+ chifukwa panalibe wina wamkulu kwa iye amene akanamulumbirira.