Ekisodo 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zitatero Mose anauza Yoswa* kuti:+ “Tisankhire amuna, ndipo upite nawo+ kukamenyana ndi Aamaleki. Mawa ndikaima pamwamba pa phiri nditagwira ndodo ya Mulungu woona m’dzanja langa.”+ Numeri 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Tenga ndodoyo,+ ndipo iwe ndi m’bale wako Aroni, musonkhanitse khamu lonse la anthuwo. Muuze thanthwe pamaso pawo kuti litulutse madzi. Utulutse madzi m’thanthweli kuti upatse khamulo, kuti limwe limodzi ndi ziweto zawo.”+
9 Zitatero Mose anauza Yoswa* kuti:+ “Tisankhire amuna, ndipo upite nawo+ kukamenyana ndi Aamaleki. Mawa ndikaima pamwamba pa phiri nditagwira ndodo ya Mulungu woona m’dzanja langa.”+
8 “Tenga ndodoyo,+ ndipo iwe ndi m’bale wako Aroni, musonkhanitse khamu lonse la anthuwo. Muuze thanthwe pamaso pawo kuti litulutse madzi. Utulutse madzi m’thanthweli kuti upatse khamulo, kuti limwe limodzi ndi ziweto zawo.”+