Deuteronomo 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Kenako ndinatembenuka ndi kutsika m’phirimo pamene phirilo linali kuyaka moto,+ ndipo miyala iwiri ya pangano inali m’manja mwanga.+
15 “Kenako ndinatembenuka ndi kutsika m’phirimo pamene phirilo linali kuyaka moto,+ ndipo miyala iwiri ya pangano inali m’manja mwanga.+