Numeri 16:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 “Amuna inu, chokani pakati pa khamuli kuti ndilifafanize kamodzi n’kamodzi.”+ Atamva zimenezi, iwo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi.+ Salimo 73:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Haa! M’kanthawi kochepa, iwo akhala chinthu chodabwitsa.+Afika pamapeto awo ndipo atha chifukwa cha masoka owagwera modzidzimutsa!
45 “Amuna inu, chokani pakati pa khamuli kuti ndilifafanize kamodzi n’kamodzi.”+ Atamva zimenezi, iwo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi.+
19 Haa! M’kanthawi kochepa, iwo akhala chinthu chodabwitsa.+Afika pamapeto awo ndipo atha chifukwa cha masoka owagwera modzidzimutsa!