Ekisodo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mulungu anapitiriza kuti: “Ngati sakakukhulupirira ndi kulabadira chizindikiro choyamba, akakhulupirira chizindikiro chachiwirichi.+
8 Mulungu anapitiriza kuti: “Ngati sakakukhulupirira ndi kulabadira chizindikiro choyamba, akakhulupirira chizindikiro chachiwirichi.+