Ekisodo 25:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri, nsalu zabwino kwambiri, ndi ubweya wa mbuzi.+ Ekisodo 26:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Upange nsalu za ubweya wa mbuzi+ zoyala pachihema chopatulika. Upange nsalu 11.
4 ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri, nsalu zabwino kwambiri, ndi ubweya wa mbuzi.+