Ekisodo 26:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Upangenso mipiringidzo ya mtengo wa mthethe,+ mipiringidzo isanu yogwira mafelemu a mbali imodzi ya chihema chopatulika.
26 “Upangenso mipiringidzo ya mtengo wa mthethe,+ mipiringidzo isanu yogwira mafelemu a mbali imodzi ya chihema chopatulika.