Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 16:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Uza Aroni m’bale wako, kuti asamalowe konse m’malo oyera+ kuseri kwa nsalu yotchinga,+ patsogolo pa chivundikiro cha Likasa, kuopera kuti angafe,+ chifukwa ine ndidzaonekera mu mtambo+ pamwamba pa chivundikirocho.+

  • Levitiko 16:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Ndiyeno azitenga ena mwa magazi a ng’ombe yamphongoyo,+ ndi kuwadontheza ndi chala chake patsogolo pa chivundikiro, chakum’mawa. Azidontheza+ magaziwo ndi chala chake maulendo 7 patsogolo pa chivundikirocho.+

  • 1 Mbiri 28:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Atatero, Davide anapatsa Solomo mwana wake mapulani akamangidwe+ ka khonde+ ndi nyumba zake, zipinda zake zosungiramo katundu,+ zipinda zake zakudenga,*+ zipinda zake zamkati zosalowa kuwala kwambiri, ndi nyumba yokhalamo chivundikiro chophimba machimo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena