Ekisodo 25:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ulipangirenso felemu, muyezo wake chikhatho* chimodzi m’lifupi mwake. Felemuli lizungulire tebulo lonse ndipo upange mkombero wagolide pafelemulo.+
25 Ulipangirenso felemu, muyezo wake chikhatho* chimodzi m’lifupi mwake. Felemuli lizungulire tebulo lonse ndipo upange mkombero wagolide pafelemulo.+