Ekisodo 25:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Tebulolo ulipangire mphete zinayi zagolide ndi kuziika m’makona ake anayi mmene muli miyendo yake inayi.+
26 Tebulolo ulipangire mphete zinayi zagolide ndi kuziika m’makona ake anayi mmene muli miyendo yake inayi.+