Levitiko 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Mose anatenga mafuta odzozera n’kudzoza chihema chopatulika+ ndi zonse zimene zinali mkati mwake, n’kuzipatula. Numeri 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa tsiku limene Mose anamaliza kumanga chihema chopatulika,+ anachidzoza+ n’kuchipatula, limodzi ndi zipangizo zake zonse, komanso guwa lansembe ndi ziwiya zake zonse. Zonse anazidzoza n’kuzipatula.+
10 Ndiyeno Mose anatenga mafuta odzozera n’kudzoza chihema chopatulika+ ndi zonse zimene zinali mkati mwake, n’kuzipatula.
7 Pa tsiku limene Mose anamaliza kumanga chihema chopatulika,+ anachidzoza+ n’kuchipatula, limodzi ndi zipangizo zake zonse, komanso guwa lansembe ndi ziwiya zake zonse. Zonse anazidzoza n’kuzipatula.+