Ekisodo 29:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Choncho ndidzakhala pakati pa ana a Isiraeli, ndipo ndidzakhala Mulungu wawo.+ Deuteronomo 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyenda limodzi nanu kuti akumenyereni nkhondo ndi kukupulumutsani kwa adani anu.’+
4 chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyenda limodzi nanu kuti akumenyereni nkhondo ndi kukupulumutsani kwa adani anu.’+