Numeri 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ana a Kohati,+ malinga ndi mayina a mabanja awo, anali Amuramu, Izara,+ Heburoni ndi Uziyeli. 1 Mbiri 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Kohati+ analipo anayi. Panali Amuramu, Izara,+ Heburoni+ ndi Uziyeli.+