Numeri 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma ana a Kora sanafe.+ 1 Mbiri 6:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Zefaniya anali mwana wa Tahati, Tahati anali mwana wa Asiri, Asiri anali mwana wa Ebiasafu,+ Ebiasafu anali mwana wa Kora,+
37 Zefaniya anali mwana wa Tahati, Tahati anali mwana wa Asiri, Asiri anali mwana wa Ebiasafu,+ Ebiasafu anali mwana wa Kora,+