Ekisodo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako iye anati: “Iponye pansi.” Anaiponya pansi ndipo inasanduka njoka.+ Pamenepo Mose anayamba kuthawa.
3 Kenako iye anati: “Iponye pansi.” Anaiponya pansi ndipo inasanduka njoka.+ Pamenepo Mose anayamba kuthawa.