Ekisodo 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako Aiguputo onse anayamba kukumba zitsime m’mphepete mwa mtsinje wa Nailo, kuti apeze madzi akumwa, chifukwa sakanatha kumwa madzi a mumtsinje wa Nailo.+
24 Kenako Aiguputo onse anayamba kukumba zitsime m’mphepete mwa mtsinje wa Nailo, kuti apeze madzi akumwa, chifukwa sakanatha kumwa madzi a mumtsinje wa Nailo.+