Miyambo 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Wochenjera ndi amene amati akaona tsoka amabisala,+ koma anthu osadziwa zinthu amangopitabe ndipo amalangidwa.+ Yona 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu a ku Nineve anayamba kukhulupirira Mulungu+ ndipo anayamba kulengeza kuti aliyense, popanda wotsala, asale kudya ndipo avale ziguduli.*+
3 Wochenjera ndi amene amati akaona tsoka amabisala,+ koma anthu osadziwa zinthu amangopitabe ndipo amalangidwa.+
5 Anthu a ku Nineve anayamba kukhulupirira Mulungu+ ndipo anayamba kulengeza kuti aliyense, popanda wotsala, asale kudya ndipo avale ziguduli.*+